nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/06.txt

1 line
189 B
Plaintext

\v 6 Niatsegula chiseko cha wokondewa wanga, koma okondewa wanga anapidamuka naku yenda. Mutima wanga unagwa pamene anakamba. Ninamufunafuna, koma sinamupeza; Ninamuitana, koma sananiyanke.