nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/03.txt

1 line
361 B
Plaintext

\v 3 Mkazi wolankhula yekha Ngati mtengo wa apurikoti pakati pa mitengo ya m'nkhalango, momwemonso wokondedwa wanga pakati pa anyamata. Ndimakhala pansi pamthunzi wake mosangalala kwambiri, ndipo zipatso zake ndi zotsekemera pakumva kwanga. \v 4 Anandibweretsa kunyumba ya vinyo, ndipo chikwangwani chake pa ine chinali chikondi. Mkazi amalankhula ndi mwamunayo