nya-x-nyanja_sng_text_reg/06/08.txt

1 line
345 B
Plaintext

\v 8 Pali mafumukazi makumi asanu na imodzi, na bakazi bafana bosabelengeka. \v 9 Nkhunda yanga, ilibe choipa, ndiye yeka; ndiye mwana mukazi umodzi yeka waba mai bake; ndiye mwana eka mukazi wamene anabala; Basikana anamuwona ndipo anamuitana odalisika; mfumukazi na azimai adamuwonanso, ndipo adamtamanda: Zomwe mfumukazi ndi adzakazi adanena