\v 16 Okondewa wanga ni wanga, ndipo ine ndine wake; adyela pakati pa maluba mwachisangalalo \v 17 Yenda, wokondewa wanga, mphepo yamutandakucha isanabwele na chiuviliuvili chisana yende . Chokani; khala ngati mphoyo, kapena nswala pa mapiri olimba.