1 line
388 B
Plaintext
1 line
388 B
Plaintext
\v 8 Pali mafumukazi makumi asanu ndi limodzi, adzakazi makumi asanu ndi atatu, ndi atsikana osawerengeka. \v 9 Nkhunda yanga, yosadetsedwa, ndiyo yokhayo; ndiye mwana wamkazi m'modzi yekha wa amake; ndiye wokondedwa kwambiri mwa mkazi amene adamubala. Atsikana anamuwona ndipo anamutcha wodala; mfumukazi ndi adzakazi adamuwonanso, ndipo adamtamanda: Zomwe mfumukazi ndi adzakazi adanena |