nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/03.txt

1 line
204 B
Plaintext

\v 3 "Navula mukanjo wanga; niyenera futi kuuvala? Nasuka menendo yanga; kodi niyafipise?" \v 4 Okondewa wanga anagenesa kwanja kwake pa nyumba ya chiseko, ndipo mutima wanga unakhudziwa chifukwa cha eve.