nya-x-nyanja_sng_text_reg/03/10.txt

1 line
372 B
Plaintext

\v 10 Nsanamira zake zinali za siliva; kubuyo kwake kwenze kwagolide, na mpando wa nyula zofiirira. Mkati mwake munakongoletsewa na chikondi na bana bakazi ba ku Yerusalemu. \v 11 Yedani bana ba kazi baku Ziyoni, ndipo yang'anani Mfumu Solomo, letani chisote chachifumu chimene amayi bake banamvelika pa tsiku yacikwati chake, pa siku ija. ya chisangalalo cha mtima wake.