nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/12.txt

1 line
288 B
Plaintext

\v 12 Maluwa yaonekela paziko lapansi; ntawi yodulia na kuimba kwa nyoni yafika, ndipo phokoso ya nkhunda yamveka mudziko yatu. \v 13 Mutengo wa mkuyu yapya nkhuyu wake yobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; zipereka fungo yake. Nyamuka, okodewa wanga, wokongola wanga, tiye tiziyenda.