|
\v 3 Mabere ako awiri ali ngati ana awiri amapasa a insa. \v 4 Khosi lako lili ngati nsanja yaminyanga ya njovu; maso ako ali ngati mayiwe a ku Hesiboni, pafupi ndi chipata cha Bath Rabbim. Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni yomwe imayang'ana ku Damasiko. |