\v 8 Mwamuna akuyankhula ndi mkazi Ngati simukudziwa, wokongola kwambiri pakati pa akazi onse, tsatirani njira za nkhosa zanga, ndipo odyetserani ana anu a mbuzi pafupi ndi mahema a abusa.