nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/05.txt

1 line
350 B
Plaintext

\v 5 Ndine wakuda koma wokondedwa, ana akazi inu a ku Yerusalemu; Ndidetsedwa ngati mahema a Kedara, okongola ngati nsalu za Solomo. \v 6 Musandiyang'ane chifukwa ndili ndi mdima, chifukwa dzuwa landiwotcha. Ana aamuna anga anakwiya nane; Anandiyika woyang'anira minda yamphesa, koma sindinasunge munda wanga wamphesa. Mkazi akulankhula ndi mwamunayo