nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/10.txt

1 line
133 B
Plaintext

\v 10 Wokondewa wanga ananikabisa kuti, uka, bwenzi ; wokongola wanga, tiye, \v 11 tiwone, kuti dzinja lapita, mvula yapita, natha.