nya-x-nyanja_sng_text_reg/03/06.txt

1 line
274 B
Plaintext

\v 6 Mkazi akudziyankhulila yekha 6Ndi ciani cikukwera kucokera kucipululu ngati utsi, wakudzola ndi mure, ndi lubani, ndi ufa wathunthu wogulitsidwa ndi amalonda? \v 7 Taonani, ndi kama wa Solomo; Ankhondo makumi asanu ndi limodzi akuzungulira, Amuna amphamvu a mu Israeli.