\v 2 Okondewa wanga ayenda kumunda wake, po gona zonunkhila, kuti udye munda naku kuikapamozi maluba. \v 3 Ndine wa okondewa wanga, ndipo wokondewa wanga ni wanga; Akudya msipu pakati pa maluba na chisangalalo.