nya-x-nyanja_sng_text_reg/04/12.txt

1 line
342 B
Plaintext

\v 12 Mlongo wanga, mkwatibwi wanga ndi munda wotsekedwa, munda wotsekedwa, kasupe wotsekedwa. \v 13 Nthambi zanu ndi munda wa makangaza wokhala ndi zipatso zabwino kwambiri, ndi zipatso za henna ndi nado, \v 14 nado ndi safironi, kalamusi ndi sinamoni wokhala ndi mitundu yonse ya zonunkhiritsa, mure ndi aloye ndi zonunkhira zabwino koposa.