nya-x-nyanja_sng_text_reg/04/04.txt

1 line
227 B
Plaintext

\v 4 Khosi lako lili ngati nsanja ya Davide yomangidwa m'mizere yamiyala, yokhala ndi zishango chikwi pa iyo, zishango zonse za ankhondo. \v 5 Mabere ako awiri ali ngati ana awiri, amapasa a insa, akudya msipu pakati pa maluwa.