nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/08.txt

1 line
253 B
Plaintext

\v 8 Pali phokoso kwa wokondedwa wanga! Mverani, apa abwera, akudumpha pamapiri, nakujumpha pamapiri. \v 9 Wokondewa wanga ali ngati mbawala kapena mwana wa mphoyo; onani, wayimirira kuseri kwa khoma lathu, akuyang'anisisa pazenera, asuzumira pazenera.