nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/16.txt

1 line
208 B
Plaintext

\v 16 Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo Mvera, ndiwe wokongola, wokondedwa wanga, ndiwe wokongola bwanji. \v 17 Zomera zobiriwira ndi kama wathu. Matabwa a nyumba yathu ndi mkungudza; Mitengo yathu ili yabwino.