nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/12.txt

1 line
291 B
Plaintext

\v 12 Maluwa yaonekera paziko lapansi; nthawi yodulira na kuimba kwa nyoni yafika, ndipo phokoso ya nkhunda ylamveka m'dziko yathu. \v 13 Mtengo wa mkuyu yapya nkhuyu zake zobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; amapereka fungo lawo. Nyamuka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiye tizipita.