\v 2 Meno yako yali ngati gulu ya nkhosa zikazi zongometa kumene, zobwera kuchokera kumalo osambirako. Aliyense ali ndi mapasa, ndipo palibe aliyense mwa iwo amene waferedwa.