nya-x-nyanja_sng_text_reg/06/10.txt

1 line
175 B
Plaintext

\v 10 "Ndani uyu wamene onekela ngati madakucha, okongola ngati mwezi, yowala ngati zuwa, odabwisa ngati gulu lankhondo lokhala ndi mbendera zake?" Mwamunayo amalankhula yekha