nya-x-nyanja_sng_text_reg/04/02.txt

1 line
174 B
Plaintext

\v 2 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zazikazi zongometa kumene, zobwera kuchokera kumalo osambirako. Aliyense ali ndi mapasa, ndipo palibe aliyense mwa iwo amene waferedwa.