\v 15 Miyendo yake ili ngati nsanamira za mwala wonyezimira, zoikidwa pazitsulo zagolidi woyengeka; Maonekedwe ake akunga Lebano, wokoma ngati mikungudza.