nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/12.txt

1 line
289 B
Plaintext

\v 12 Maluwa yaonekera padziko lapansi; nthawi yodulira na kuimba kwa nyoni yafika, ndipo phokosola nkhunda lamveka m'dziko lathu. \v 13 Mtengo wa mkuyu upsa nkhuyu zake zobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; amapereka fungo lawo. Nyamuka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiye tizipita.