nya-x-nyanja_sng_text_reg/04/10.txt

1 line
317 B
Plaintext

\v 10 Ndi wokongola bwanji chikondi chako, mlongo wanga, mkwatibwi wanga! Chikondi chako chiposa vinyo motani, ndi fungo labwino la zonunkhira zako kuposa zonunkhiritsa zilizonse. \v 11 Milomo yako, mkwatibwi, ikukha uchi; uchi ndi mkaka zili pansi pa lilime lako; kununkhira kwa zovala zako ndikununkhira kwa Lebano.