nya-x-nyanja_sng_text_reg/03/01.txt

1 line
281 B
Plaintext

\c 3 \v 1 Usiku nili pabedi yanga neze kulakalaka wamene moyo wanga ukonda; Ninamfunafuna, koma sininamupeze. \v 2 Ninazikambisa neka, "Niza uka naku kupyola pakati pa mzinda, kupyolela m'misewu na m'mabwalo; nizafufuza wamene moyo wanga umkonda." Ninamfunafuna koma sininamupeze.