nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/03.txt

1 line
301 B
Plaintext

\v 3 Ngati mtengo wa apurikoti pakati pa mitengo ya m'nkhalango, chimozimozi wokondewa wanga pakati pa anyamata. Nimakhala pansi pachifile chake mosangalala kwambiri, ndipo zipatso zake ni zozuna pakumvara kwanga. \v 4 Ananibweresa kunyumba ya vinyo, ndipo chikwangwani chake pa ine chinali chikondi.