nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/10.txt

1 line
179 B
Plaintext

\v 10 Okondewa wanga ni owala na maonekedwe yabwino, opambana pakati pa zikwi khumi. \v 11 Mutu wake ni golide woyengeka bwino; sisi yake ni yopobana koma yakuda ngati khwangwala.