nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/09.txt

1 line
226 B
Plaintext

\v 9 Okondewa wanga, nikulinganiza na mwana mkazi pakati pa magaleta ya Farao. \v 10 Mbovu zako ni zabwino n zokongola, mukhosi wako na zokongoletsa zo kolobeka. \v 11 Tikupangira zokongoletsera zagolide na zomangira zasiliva.