nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/14.txt

1 line
218 B
Plaintext

\v 14 Nkhunda yanga, m'matanthwe ya thanthwe, muchisinsi cha m'matanthwe chamuma piri yobisamilako, nkhope yanu. Ndimve mawu ako, chifukwa mawu ako ndi okoma, nkhope yako ndi yokongola. "Mkazi akuyankhula ndi mwamunayo