nya-x-nyanja_sng_text_reg/08/08.txt

1 line
180 B
Plaintext

\v 8 Abale a mkaziyo amalankhulana pakati pawo Tili ndi mlongo wathu wamng'ono, ndipo mabere ake sanakulebe. Kodi tingatani kwa mlongo wathu patsiku lomwe adzalonjezedwe kukwatiwa?