nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/09.txt

1 line
190 B
Plaintext

\v 9 Kodi bwenzi lako liposa mwamuna wina wokondedwa, iwe wokongola kwambiri mwa akazi onse? Chifukwa chiyani wokondedwa wako aposa wokondedwa wina, kuti utifunse ife titenge lumbiro lotere?