nya-x-nyanja_sng_text_reg/07/07.txt

1 line
275 B
Plaintext

\v 7 Kutalika kwako kuli ngati mtengo wa kanjedza, ndipo mabere ako ali ngati masango a zipatso. \v 8 Ndinati, "Ndikufuna kukwera mtengo wa mgwalangwawo; ndigwira nthambi zake." Mabere ako akhale ngati zipatso za mphesa, Ndipo fungo la m'mphuno mwako likhale ngati apurikoti.