\v 10 Wokondewa wanga ni owala ni ofiira, opambana pakati pa zikwi khumi. \v 11 Mutu wake ni golide woyengeka bwino; sisi yake ni yopobana koma yakuda ngati khwangwala.