nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/09.txt

1 line
193 B
Plaintext

\v 9 Nanga bwenzi wako apitililapo mwamuna wina wokondewa, iwe wokongola kwambiri pali bakazi bonse? Chifukwa chani wokondewa wako apitilila wokondewa bena, kuti uifunse ife tenga lumbiro yaso?