1 line
314 B
Plaintext
1 line
314 B
Plaintext
\v 12 Mlongo wanga, muwatibwi wanga ni munda ovaliwa, munda ovaliwa, kasupe ovaliwa. \v 13 Misambo zanu na munda wa makangaza na zipaso zabwino kwambiri, ni zipaso za henna ni nado, \v 14 nado na safironi, kalamusi na sinamoni yokhala na mitundu yonse ya zonunkhiritsa, mure ndi aloye na zonunkhira zabwino koposa. |