nya-x-nyanja_sng_text_reg/02/05.txt

1 line
209 B
Plaintext

\v 5 Nitsitsimutseni ine makeke a mphesa ndipo munitsisimuse na maapurikoti, chifukwa nalema na chikondi. \v 6 Kwanja kwake kwamanzere kuli pansi kwa mutu wanga, ndipo kwanja kwake kwamanja kwanikumbatira ine.