nya-x-nyanja_sng_text_reg/08/11.txt

1 line
333 B
Plaintext

\v 11 Solomoni anali na munda wamphesa ku Baal Hamoni. Anapasa munda kuli beve bamene bosamalila. Aliyense anali kuyenela kubwelesa ndalama zasiliva zokwana 1,000 zazi paso. \v 12 Munda wanga wamphesa, wanga wamene, uli pamenso panga; masekeli zikiwi chimodzi ni yako, Solomoni, na masekeli mazana ya bili ni ya osunga zipatso zake.