nya-x-nyanja_sng_text_reg/06/11.txt

1 line
276 B
Plaintext

\v 11 Ndidatsikira kumunda wamitengo kuti ndikawone kakulidwe kamene kali m'chigwacho, kuti ndikawone ngati mipesa idaphukira, kapena ngati makangaza ali pachimake. \v 12 Ndinali wokondwa kwambiri kuti ndimamva kuti ndinkakwera galeta la kalonga abwenzi akuyankhula ndi mayiyo