nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/16.txt

1 line
175 B
Plaintext

\v 16 Mvea, ndiwe wokongola, wokondedwa wanga, ndiwe wokongola bwanji.zomera zobiribila ndi kama yathu. \v 17 mupanda wa nyumba yathu ni mkungudza; Mitengo yathu ili yabwino.