nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/02.txt

1 line
254 B
Plaintext

\v 2 Ninali mutulo, koma mutima wanga unali menso. Pali phokoso ya wokondewa wanga agogoda naku kamba kuti, "Nisegulire, mlongo wanga, okondewa wanga, nkhunda yanga, wanga osadesewa, pakuti mutu wanga wanyowa na mame, stsi yanga ni chinyontho cha usiku."