nya-x-nyanja_sng_text_reg/03/03.txt

1 line
367 B
Plaintext

\v 3 Malonda ananipeza pamene anali kuzungulila mizinda. Nina funsa kuti, "Kodi mwaonako wamene moyo wanga nikonda?" \v 4 Panapita ka ntawi pang'ono nisanampitilile kwakuti nina mupeza wamene moyo wanga uma mukonda. Ninamu gwililila ndipo sinimu lekelako kuyenda kufikila ninamuleta 'munyumba yaba amayi banga, mu chipinda chogona cha amene ananipatsa bananibala.