nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/12.txt

1 line
253 B
Plaintext

\v 12 Mfumu ili gone pabedi pake, nade wanga anali kuchosa kununkila kwake. \v 13 Okondewa wanga alimonga tumba ya mule yamene imagona pakati pa mabele yanga. \v 14 Okondewa wanga ali ngati kuli ine sango Ya maluba ya heni mumuda yamphesa ya En-Gedi.