\v 3 Malonda ananipeza pamene anali kuzungulira mzinda. Ninamfunsa kuti, "Kodi mwaonako wamene moyo wanga nikonda?" \v 4 Panapita kanthawi pang'ono nisanampitilile kwakuti nina mupeza wamene moyo wanga umamukonda. Ninamugwirilila ndipo sinimulekeleko kuyenda kufikira ninamuleta 'munyumba yaba amayi banga, mchipinda chogona cha amene ananipatsa bananibala.