\v 10 ndine wa wokondewa wanga, ndipo amanilakalaka. \v 11 Bwela, okondewa wanga, tiye tichoke muziko; tiye tika gone mumuzi.