\v 7 Kutalimpa kwako kuli ngati mtengo wa kanjeza, ndipo mabele yako yali ngati gulu ya zipatso. \v 8 Ninakamba kuti, "Nifuna kukwela mutengo wa kanjeza; nizagwila misabo zake." Mabele yako yakhale ngati zipatso za mphesa, Ndipo fungoyla mphuno yako ikhale ngati apulikoti.