\c 6 \v 1 Okondedwa wako ayenda kuti, iwe wokongola kwambili pali bakazi onse? Okondewa wanu ayenda kuti, kuti timusakile pamodzi na iwe?