\v 7 Olonda ananipeza pamene anali kuzungulukila muzinda. Bananimenya nakunipanga viloda; olonda pamakoma anani poka chovala changa.