\v 6 Mpaka mbandakucha na mutunzi kusana tabe, nizayenda phili ya myrra na kuchulu cha lubani. \v 7 Ndiwe wokongola munjia zonse, okondewa wanga ndipo palibe choipa pali iwe.