\v 6 Mpaka mbandakucha ndi mithunzi ithawe, ndipita kuphiri la mure ndi kuphiri la lubani. \v 7 Ndiwe wokongola m'njira zonse, wokondedwa wanga ndipo palibe chilema mwa iwe.